Kusiyana Kwa Baibulo Ndi Qur'an
| Baibulo | Qur'an |
| Limanena kuti Mulungu ndi m’modzi, komanso utatu wa Umulungu, (Yesaya 43:10; Mateyu 28:19; 2 Akolinto 13:14). | Imanena kuti Mulungu ndi m’modzi (5:73; 112:1-4), koma imakana za utatu wa Umulungu (5:73). |
| Limanena kuti Yesu ndi Mulungu m’thupi (Akolose 2:9). | Imanena kuti Yesu si mwana wa Mulungu (5:17, 75). |
| Limanena kuti Yesu anapachikidwa pa mtanda (1 Petro 2:24). | Imanena kuti Yesu sanapachikidwe pa mtanda (4:157). |
| Limanena kuti Yesu anuka kwa akufa (Yohane 2:19). | Imanena kuti Yesu sanapachikidwe pa mtanda (4:157). |
| Limanena kuti Yesu anali mwana wa Mulungu (Maliko 1:1). | Imanena kuti sanali mwana wa Mulungu (9:30). |
| Limanena kuti Mzimu Woyera ndi wachitatu mu Umulungu ndipo amachitira umboni za Yesu (Yohani 14:26; 15:26). | Imanena kuti Gabriel ndi M’ngelo (2:97; 16:102). |
| Limanena kuti munthu adzapulumutsidwa ndi chisomo kupyolera m’chikhulupiliro (Aefeso 2:8,9). | Imanena kuti chipulumutso tidzachipeza pochita zachifundo komanso ntchito zathu (3:135; 7:8-9; 21:47; 49:14; 66:8-9). |
| Limanena kuti Satana ndi m’ngelo wakugwa (wochimwira Mulungu) Yesaya 14:12-15) | Imanena kuti Satana si m’ngelo wakugwa(wochimwa) komatu Jinn wakugwa(wochimwa) (2:34; 7:12; 15:27; 55:15). |
| Limanena kuti munthu ndi wochimwa(wakugwa mu uchimo), (Aroma 3:23). | Imanena kuti munthu ndi wosachimwa (wabwino). |
| Limanena kuti ophunzira a Yesu anali akhristu (Machitidwe 11:26). | Imannena kuti ophunzira a Yesu anali anadzitcha okha Asilamu (15:111). |
| Limanena kuti poyamba chipembedzo chinali kuchitika pa Sabata (Exsodo 20). Ndipo kenako tsiku loyamba la Sabata(la Mulungu) (Aroma 14:5-6; Machitidwe 20:7; 1 Akolinto 16:1-2). | Imanena kuti Asilamu ayenera kepembedza la chisanu (62:9). |
| Limanena kuti m’Baibulo munalembedwa zizizwitsa zambiri. | Mulibe zozizwizitsa kupaturapo kuti Quraniyo ndi bukhu lozizwitsa. |
| Limanena kuti m’Baibulo muli maulosi ambiri. | Mulibe ulosi. |
NB. Ndidzakhala ndikukupatsirani zinanso zikapezeka.
|
|
|
CARM ison |
| Tweet |
| Follow @Carmorg |
Apologetics
- Apologetics
- Apologetics Dialogues
- CARM Radio
- Cut and Paste Information
- Discussion Boards
- Email and Responses
- Evidence and Answers
- Heresies
- Lost Books
- Objections and Answers
- Online Schools
- Preachers and Teachers
- Recommended Websites
- Research Links
- Responding to Critics
- Verses Examined - OT
- Verses Examined - NT
- Women in Ministry
- Women's Issues
Christian Life
Secular Movements
Questions
- About Angels
- About Apologetics
- About Baptism
- About the Bible
- About Bible Verses
- About the Church
- About Christianity
- About Demons
- About Doctrine
- About End Times
- About Ethics
- About Evangelism
- About God
- About Heresies
- About The Holy Spirit
- About Jesus
- About Man
- About Marriage
- About the Occult
- About Pastors
- About People
- About Prayer
- About Philosophy
- About Religions
- About Salvation
- About Sanctification
- About Science
- About Sexuality
- About Sin
- About Theology
- Other Questions
- Skeptics Ask
Help CARM by Liking It!
See Also
CARM ONLINE SCHOOLS
A lot of knowledge and an easy way to learn it.
15%
Discount off of Logos Bible Program.
CARM highly recommends using the Logos Bible Research Program. It is what
we use. It is the best in the world.
Just go to
http://www.logos.com/carm.
Use the coupon code of CARM6.

